Salimo 110:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 110 Yehova wauza Ambuye wanga kuti:+“Khala kudzanja langa lamanja+Kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako.”+ Aheberi 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma munthu ameneyu anapereka nsembe imodzi yamachimo kwamuyaya,+ ndipo anakhala pansi kudzanja lamanja la Mulungu.+
110 Yehova wauza Ambuye wanga kuti:+“Khala kudzanja langa lamanja+Kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako.”+
12 Koma munthu ameneyu anapereka nsembe imodzi yamachimo kwamuyaya,+ ndipo anakhala pansi kudzanja lamanja la Mulungu.+