Aheberi 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Onsewa anafa ali ndi chikhulupiriro,+ ngakhale kuti sanaone kukwaniritsidwa kwa malonjezowo.+ Koma anawaona ali patali+ ndi kuwalandira, ndipo analengeza poyera kuti iwo anali alendo ndi osakhalitsa m’dzikolo.+
13 Onsewa anafa ali ndi chikhulupiriro,+ ngakhale kuti sanaone kukwaniritsidwa kwa malonjezowo.+ Koma anawaona ali patali+ ndi kuwalandira, ndipo analengeza poyera kuti iwo anali alendo ndi osakhalitsa m’dzikolo.+