Aefeso 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munali kuyenda m’zimenezo mogwirizana ndi nthawi*+ za m’dzikoli, momveranso wolamulira+ wa mpweya umene umalamulira zochita za anthu. Mpweya umenewu, kapena kuti kaganizidwe kameneka,+ tsopano kakugwira ntchito mwa ana a kusamvera.+
2 Munali kuyenda m’zimenezo mogwirizana ndi nthawi*+ za m’dzikoli, momveranso wolamulira+ wa mpweya umene umalamulira zochita za anthu. Mpweya umenewu, kapena kuti kaganizidwe kameneka,+ tsopano kakugwira ntchito mwa ana a kusamvera.+