Aefeso 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiponso, Mulungu anapangitsa inuyo kukhala amoyo pamene munali akufa chifukwa cha zolakwa zanu ndi machimo anu.+ Aefeso 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 anatikhalitsa amoyo pamodzi ndi Khristu, ngakhale kuti tinali akufa m’machimo,+ (pakuti inu mwapulumutsidwa chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu)+ Aefeso 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma tsopano mogwirizana ndi Khristu Yesu, inu amene pa nthawi ina munali kutali, mwakhala pafupi chifukwa cha magazi+ a Khristu.
2 Ndiponso, Mulungu anapangitsa inuyo kukhala amoyo pamene munali akufa chifukwa cha zolakwa zanu ndi machimo anu.+
5 anatikhalitsa amoyo pamodzi ndi Khristu, ngakhale kuti tinali akufa m’machimo,+ (pakuti inu mwapulumutsidwa chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu)+
13 Koma tsopano mogwirizana ndi Khristu Yesu, inu amene pa nthawi ina munali kutali, mwakhala pafupi chifukwa cha magazi+ a Khristu.