Yohane 18:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Yesu anayankha kuti:+ “Ufumu wanga suli mbali ya dziko lino.+ Ufumu wanga ukanakhala mbali ya dziko lino, atumiki anga akanamenya nkhondo+ kuti ndisaperekedwe kwa Ayuda. Koma ufumu wanga si wochokera pansi pano ayi.” Aroma 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 chifukwa kuika maganizo pa zinthu za thupi ndiko udani+ ndi Mulungu, popeza thupi siligonjera+ chilamulo cha Mulungu, ndipotu kunena zoona, silingachigonjere. 1 Yohane 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Musamakonde dziko kapena zinthu za m’dziko.+ Ngati wina akukonda dziko, ndiye kuti sakonda Atate.+
36 Yesu anayankha kuti:+ “Ufumu wanga suli mbali ya dziko lino.+ Ufumu wanga ukanakhala mbali ya dziko lino, atumiki anga akanamenya nkhondo+ kuti ndisaperekedwe kwa Ayuda. Koma ufumu wanga si wochokera pansi pano ayi.”
7 chifukwa kuika maganizo pa zinthu za thupi ndiko udani+ ndi Mulungu, popeza thupi siligonjera+ chilamulo cha Mulungu, ndipotu kunena zoona, silingachigonjere.
15 Musamakonde dziko kapena zinthu za m’dziko.+ Ngati wina akukonda dziko, ndiye kuti sakonda Atate.+