-
Ekisodo 8:9, 10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndiyeno Mose anauza Farao kuti: “Munene ndinu kuti ndikachonderere liti kwa Mulungu kuti achulewa achoke kwa inu, kwa atumiki anu, anthu anu ndi mʼnyumba zanu. Achulewa adzangotsala mumtsinje wa Nailo mokha.” 10 Pamenepo Farao anayankha kuti: “Mawa.” Ndiyeno Mose anati: “Zichitika mogwirizana ndi zimene mwanena kuti mudziwe kuti palibenso wina wofanana ndi Yehova Mulungu wathu.+
-