-
Ekisodo 16:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Mʼchipululumo gulu lonse la Aisiraeli linayamba kungʼungʼudzira Mose ndi Aroni.+ 3 Aisiraeliwo ankauza Mose ndi Aroni kuti: “Zikanakhala bwino dzanja la Yehova likanatiphera mʼdziko la Iguputo, kumene tinkadya nyama+ ndi mkate nʼkukhuta. Mʼmalomwake mwatibweretsa mʼchipululu muno kuti muphetse mpingo wonsewu ndi njala.”+
-