Ekisodo 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho anthu anayamba kungʼungʼudza motsutsana ndi Mose+ kuti: “Timwa chiyani?” 1 Akorinto 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zinthu zimenezi ndi zitsanzo kwa ife, kuti nafenso tisamalakelake zinthu zoipa ngati mmene iwo anachitira.+ 1 Akorinto 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tisakhalenso ongʼungʼudza, ngati mmene ena a iwo anachitira,+ nʼkuphedwa ndi mngelo wowononga.+
6 Zinthu zimenezi ndi zitsanzo kwa ife, kuti nafenso tisamalakelake zinthu zoipa ngati mmene iwo anachitira.+