Yoswa 24:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako munawoloka Yorodano+ nʼkufika ku Yeriko.+ Atsogoleri a* ku Yeriko, omwe ndi Aamori, Aperezi, Akanani, Ahiti, Agirigasi, Ahivi ndi Ayebusi, anayamba kumenyana nanu, koma ine ndinawapereka mʼmanja mwanu.+
11 Kenako munawoloka Yorodano+ nʼkufika ku Yeriko.+ Atsogoleri a* ku Yeriko, omwe ndi Aamori, Aperezi, Akanani, Ahiti, Agirigasi, Ahivi ndi Ayebusi, anayamba kumenyana nanu, koma ine ndinawapereka mʼmanja mwanu.+