Yobu 28:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno anauza munthu kuti: ‘Tamvera, kuopa Yehova ndi nzeru,+Ndipo kupewa zoipa ndiko kumvetsa zinthu.’”+ Miyambo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kuopa Yehova ndi chiyambi cha kudziwa zinthu.+ Zitsiru zokha ndi zimene zimanyoza nzeru komanso malangizo.+ Miyambo 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso mawu achinyengo.+ 1 Petulo 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Muzilemekeza anthu amitundu yonse.+ Muzikonda gulu lonse la abale,+ muziopa Mulungu+ komanso muzilemekeza mfumu.+
28 Ndiyeno anauza munthu kuti: ‘Tamvera, kuopa Yehova ndi nzeru,+Ndipo kupewa zoipa ndiko kumvetsa zinthu.’”+
7 Kuopa Yehova ndi chiyambi cha kudziwa zinthu.+ Zitsiru zokha ndi zimene zimanyoza nzeru komanso malangizo.+
13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso mawu achinyengo.+
17 Muzilemekeza anthu amitundu yonse.+ Muzikonda gulu lonse la abale,+ muziopa Mulungu+ komanso muzilemekeza mfumu.+