Genesis 29:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anakhalanso woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Tsopano nditamanda Yehova.” Choncho Leya anamupatsa mwanayo dzina lakuti Yuda.*+ Atabereka mwana ameneyu, anasiya kaye kubereka. Genesis 46:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Yuda+ anali Ere, Onani, Shela,+ Perezi+ ndi Zera.+ Koma Ere ndi Onani anafera kudziko la Kanani.+ Ana a Perezi anali Hezironi ndi Hamuli.+ Numeri 2:3, 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amene azimanga msasa wawo kumʼmawa kotulukira dzuwa ndi gulu la mafuko atatu la Yuda ndi magulu awo.* Mtsogoleri wa ana a Yuda ndi Naasoni,+ mwana wa Aminadabu. 4 Asilikali ake amene analembedwa mayina alipo 74,600.+ 1 Mbiri 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ngakhale kuti Yuda+ anali wamphamvu pakati pa azichimwene ake ndiponso kubanja lake kunachokera wodzakhala mtsogoleri,+ udindo wa woyamba kubadwa unali wa Yosefe. Mateyu 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Abulahamu anabereka Isaki.+Isaki anabereka Yakobo.+Yakobo anabereka Yuda+ ndi azichimwene ake. Aheberi 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tonse tikudziwa kuti Ambuye wathu anachokera ku fuko la Yuda+ koma Mose sananenepo kuti ansembe adzachokera mu fuko limeneli.
35 Anakhalanso woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Tsopano nditamanda Yehova.” Choncho Leya anamupatsa mwanayo dzina lakuti Yuda.*+ Atabereka mwana ameneyu, anasiya kaye kubereka.
12 Ana a Yuda+ anali Ere, Onani, Shela,+ Perezi+ ndi Zera.+ Koma Ere ndi Onani anafera kudziko la Kanani.+ Ana a Perezi anali Hezironi ndi Hamuli.+
3 Amene azimanga msasa wawo kumʼmawa kotulukira dzuwa ndi gulu la mafuko atatu la Yuda ndi magulu awo.* Mtsogoleri wa ana a Yuda ndi Naasoni,+ mwana wa Aminadabu. 4 Asilikali ake amene analembedwa mayina alipo 74,600.+
2 Ngakhale kuti Yuda+ anali wamphamvu pakati pa azichimwene ake ndiponso kubanja lake kunachokera wodzakhala mtsogoleri,+ udindo wa woyamba kubadwa unali wa Yosefe.
2 Abulahamu anabereka Isaki.+Isaki anabereka Yakobo.+Yakobo anabereka Yuda+ ndi azichimwene ake. Aheberi 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tonse tikudziwa kuti Ambuye wathu anachokera ku fuko la Yuda+ koma Mose sananenepo kuti ansembe adzachokera mu fuko limeneli.
14 Tonse tikudziwa kuti Ambuye wathu anachokera ku fuko la Yuda+ koma Mose sananenepo kuti ansembe adzachokera mu fuko limeneli.