Genesis 36:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Timina anali mkazi wamngʼono wa Elifazi mwana wa Esau. Patapita nthawi, Timina anaberekera Elifazi mwana wamwamuna dzina lake Amaleki.+ Ana a Ada mkazi wa Esau anali amenewa. Ekisodo 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Aamaleki+ anabwera kudzamenyana ndi Isiraeli ku Refidimu.+ 1 Samueli 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano pita ukaphe Aamaleki+ ndiponso kuwononga+ zinthu zonse zimene ali nazo. Usakasiye aliyense.* Ukaphe+ mwamuna ndi mkazi, mwana wamngʼono ndi wakhanda, ngʼombe ndi nkhosa komanso ngamila ndi bulu.’”+
12 Timina anali mkazi wamngʼono wa Elifazi mwana wa Esau. Patapita nthawi, Timina anaberekera Elifazi mwana wamwamuna dzina lake Amaleki.+ Ana a Ada mkazi wa Esau anali amenewa.
3 Tsopano pita ukaphe Aamaleki+ ndiponso kuwononga+ zinthu zonse zimene ali nazo. Usakasiye aliyense.* Ukaphe+ mwamuna ndi mkazi, mwana wamngʼono ndi wakhanda, ngʼombe ndi nkhosa komanso ngamila ndi bulu.’”+