-
Deuteronomo 28:1, 2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 “Mukamveradi mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse amene ndikukupatsani lero, Yehova Mulungu wanu adzakukwezani ndithu pamwamba pa mitundu yonse ya padziko lapansi.+ 2 Mudzalandira madalitso onsewa ndipo zinthu zabwino zonsezi zidzakhala zanu,+ mukapitiriza kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu:
-