Levitiko 26:3, 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mukapitiriza kutsatira malangizo anga ndi kusunga malamulo anga,+ 4 ndidzakugwetserani mvula pa nthawi yake.+ Nthaka idzakupatsani chakudya,+ ndipo mitengo yamʼmunda idzakupatsani zipatso zake. Miyambo 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Madalitso a Yehova ndi amene amalemeretsa munthu,+Ndipo popereka madalitsowa Mulungu sawonjezerapo ululu.* Yesaya 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mukakhala ndi mtima wofuna kundimvera,Mudzadya zinthu zabwino za mʼdziko lanu.+
3 Mukapitiriza kutsatira malangizo anga ndi kusunga malamulo anga,+ 4 ndidzakugwetserani mvula pa nthawi yake.+ Nthaka idzakupatsani chakudya,+ ndipo mitengo yamʼmunda idzakupatsani zipatso zake.
22 Madalitso a Yehova ndi amene amalemeretsa munthu,+Ndipo popereka madalitsowa Mulungu sawonjezerapo ululu.*