Levitiko 27:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kuwonjezera pamenepa, munthu aliyense amene waperekedwa kwa Mulungu kuti awonongedwe sangathe kuwomboledwa.+ Ameneyo aziphedwa ndithu.+ Yoswa 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yoswa analanda mizinda yonse ya mafumuwa, nʼkupha mafumu ake onse ndi lupanga+ mogwirizana ndi zimene Mose, mtumiki wa Yehova, analamula. Yoswa 24:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako munawoloka Yorodano+ nʼkufika ku Yeriko.+ Atsogoleri a* ku Yeriko, omwe ndi Aamori, Aperezi, Akanani, Ahiti, Agirigasi, Ahivi ndi Ayebusi, anayamba kumenyana nanu, koma ine ndinawapereka mʼmanja mwanu.+
29 Kuwonjezera pamenepa, munthu aliyense amene waperekedwa kwa Mulungu kuti awonongedwe sangathe kuwomboledwa.+ Ameneyo aziphedwa ndithu.+
12 Yoswa analanda mizinda yonse ya mafumuwa, nʼkupha mafumu ake onse ndi lupanga+ mogwirizana ndi zimene Mose, mtumiki wa Yehova, analamula.
11 Kenako munawoloka Yorodano+ nʼkufika ku Yeriko.+ Atsogoleri a* ku Yeriko, omwe ndi Aamori, Aperezi, Akanani, Ahiti, Agirigasi, Ahivi ndi Ayebusi, anayamba kumenyana nanu, koma ine ndinawapereka mʼmanja mwanu.+