-
1 Samueli 9:16, 17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 “Mawa cha nthawi ngati ino ndidzakutumizira munthu kuchokera kudera la Benjamini.+ Udzamudzoze kuti akhale mtsogoleri wa anthu anga Aisiraeli.+ Iye adzapulumutsa anthu anga mʼmanja mwa Afilisiti, chifukwa ndaona mmene akuvutikira ndiponso ndamva kulira kwawo.”+ 17 Samueli ataona Sauli, Yehova anamuuza kuti: “Munthu amene ndinakuuza uja ndi ameneyu. Uja ndinati, ‘Ndi amene adzalamulire anthu anga.’”+
-