Yoswa 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako gulu lonse la Aisiraeli linasonkhana ku Silo,+ ndipo kumeneko anamanga chihema chokumanako,+ popeza pa nthawiyo nʼkuti atagonjetsa dzikolo.+ 1 Samueli 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthuwo atabwerera kumsasa, akulu a Isiraeli ananena kuti: “Nʼchifukwa chiyani lero Yehova walola kuti Afilisiti atigonjetse?*+ Tiyeni tikatenge likasa la pangano la Yehova ku Silo+ tizikhala nalo, kuti litipulumutse mʼmanja mwa adani athu.”
18 Kenako gulu lonse la Aisiraeli linasonkhana ku Silo,+ ndipo kumeneko anamanga chihema chokumanako,+ popeza pa nthawiyo nʼkuti atagonjetsa dzikolo.+
3 Anthuwo atabwerera kumsasa, akulu a Isiraeli ananena kuti: “Nʼchifukwa chiyani lero Yehova walola kuti Afilisiti atigonjetse?*+ Tiyeni tikatenge likasa la pangano la Yehova ku Silo+ tizikhala nalo, kuti litipulumutse mʼmanja mwa adani athu.”