8 Nditaona zimenezo, ndinathamangitsa Isiraeli wosakhulupirikayo ndipo ndinamupatsa kalata yotsimikizira kuti ukwati watha+ chifukwa anachita chigololo.+ Koma Yuda mchemwali wake, amene ndi wachinyengo, sanachite mantha. Nayenso anayamba kuchita uhule.+