Ekisodo 22:22, 23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Musamazunze mkazi wamasiye kapena mwana wamasiye* aliyense.+ 23 Ngakhale mutamuzunza pangʼono, iye nʼkundilirira, ndidzamva ndithu kulira kwake.+ Yakobo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani! Malipiro amene simunapereke kwa anthu amene anagwira ntchito yokolola mʼminda yanu akufuula ndipo Yehova* wa magulu ankhondo akumwamba wamva kufuula kopempha thandizo kwa anthu okololawo.+
22 Musamazunze mkazi wamasiye kapena mwana wamasiye* aliyense.+ 23 Ngakhale mutamuzunza pangʼono, iye nʼkundilirira, ndidzamva ndithu kulira kwake.+
4 Tamverani! Malipiro amene simunapereke kwa anthu amene anagwira ntchito yokolola mʼminda yanu akufuula ndipo Yehova* wa magulu ankhondo akumwamba wamva kufuula kopempha thandizo kwa anthu okololawo.+