2 Phiri la Ziyoni limene lili mʼdera lakutali lakumpoto,
Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka komanso anthu padziko lonse lapansi akusangalala nalo,+
Ndipo ndi mzinda wa Mfumu Yaikulu.+
3 Munsanja zake zokhala ndi mpanda wolimba,
Mulungu wasonyeza kuti iye ndi malo othawirako otetezeka.+