26 Ndiye ndinapeza izi: Mkazi amene ali ngati ukonde wosakira nyama, amene mtima wake uli ngati khoka, komanso amene manja ake ali ngati unyolo wakundende, ndi wowawa kwambiri kuposa imfa. Munthu amene amasangalatsa Mulungu woona adzamuthawa,+ koma wochimwa amagwidwa naye.+