-
Mateyu 15:5, 6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Koma inu mumanena kuti, ‘Aliyense wouza bambo ake kapena mayi ake kuti: “Chilichonse chimene ndili nacho, chimene ndikanakuthandizani nacho ndi mphatso yoti ndipereke kwa Mulungu,”+ 6 sakuyenera kuthandiza bambo ake.’ Choncho mwachititsa kuti mawu a Mulungu akhale opanda pake chifukwa cha miyambo yanu.+
-