Miyambo 3:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Usakangane ndi munthu popanda chifukwa+Ngati sanakuchitire choipa chilichonse.+ Miyambo 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Munthu woyambitsa mavuto* amayambanitsa anthu,+Ndipo wonenera anzake zoipa amalekanitsa mabwenzi apamtima.+ Miyambo 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kuyambitsa ndewu kuli ngati kuboola damu kuti madzi atulukemo.*Choncho mkangano usanabuke, chokapo.+
28 Munthu woyambitsa mavuto* amayambanitsa anthu,+Ndipo wonenera anzake zoipa amalekanitsa mabwenzi apamtima.+
14 Kuyambitsa ndewu kuli ngati kuboola damu kuti madzi atulukemo.*Choncho mkangano usanabuke, chokapo.+