Nyimbo ya Solomo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Ndiwe wokongola wokondedwa wanga. Ndiwe chiphadzuwa. Maso ako ali ngati maso a njiwa munsalu yako yophimba kumutuyo. Tsitsi lako lili ngati gulu la mbuziZimene zikuthamanga potsika mapiri a ku Giliyadi.+
4 “Ndiwe wokongola wokondedwa wanga. Ndiwe chiphadzuwa. Maso ako ali ngati maso a njiwa munsalu yako yophimba kumutuyo. Tsitsi lako lili ngati gulu la mbuziZimene zikuthamanga potsika mapiri a ku Giliyadi.+