-
Yeremiya 10:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Munthu aliyense akuchita zinthu mopanda nzeru komanso mosazindikira.
-
-
Aroma 1:21-23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Ngakhale kuti ankadziwa Mulungu, iwo sanamulemekeze monga Mulungu komanso sanamuthokoze. Mʼmalomwake anayamba kuganiza zinthu zopanda nzeru ndipo mitima yawo yopusayo inachita mdima.+ 22 Ngakhale amanena kuti ndi anzeru, iwo ndi opusa. 23 Mʼmalo molemekeza Mulungu yemwe sangafe, iwo amalemekeza zifaniziro za anthu omwe amafa komanso zifaniziro za mbalame, nyama za miyendo 4 ndiponso nyama zokwawa.+
-