-
Ezekieli 33:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Auze kuti, ‘“Pali ine Mulungu wamoyo,” akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, “Ine sindisangalala ndi imfa ya munthu woipa,+ koma ndimafuna kuti munthu woipa asinthe zochita zake+ nʼkupitiriza kukhala ndi moyo.+ Bwererani! Bwererani nʼkusiya zinthu zoipa zimene mukuchita.+ Muferenji inu a nyumba ya Isiraeli?”’+
-