-
Ezekieli 17:13, 14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kuwonjezera apo, inatenga mmodzi mwa ana* achifumu+ nʼkuchita naye pangano ndi kumulumbiritsa.+ Kenako mfumuyo inatenga anthu otchuka amʼdzikolo nʼkupita nawo kwawo+ 14 nʼcholinga choti ufumuwo ukhale waungʼono, usakhalenso wamphamvu, koma kuti ufumuwo udzapitirize kukhalapo ngati Aisiraeli atasunga pangano limene anachita.+
-