-
Mateyu 24:23, 24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Choncho munthu akadzakuuzani kuti, ‘Onani! Khristu uja ali kuno,’+ kapena, ‘Ali uko!’ musadzakhulupirire zimenezo.+ 24 Chifukwa kudzabwera anthu onamizira kuti ndi Khristu komanso aneneri abodza+ ndipo adzachita zizindikiro zamphamvu ndiponso zodabwitsa, kuti ngati nʼkotheka, adzasocheretse+ ngakhale osankhidwawo.
-