Mateyu 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu akayatsa nyale saivindikira ndi dengu, koma amaiika pachoikapo nyale ndipo imaunikira onse mʼnyumbamo.+ Maliko 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye anawauzanso kuti: “Nyale saivindikira ndi dengu* kapena kuiika pansi pa bedi, amatero ngati? Koma amaiika pachoikapo nyale,+ si choncho kodi? Luka 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Munthu akayatsa nyale saiika pamalo obisika kapena kuivindikira ndi dengu,* koma amaiika pachoikapo nyale,+ kuti amene akulowa aone kuwala. Afilipi 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 kuti mukhale opanda chifukwa chokunenezerani komanso osalakwa. Mukhale ana a Mulungu+ opanda chilema pakati pa mʼbadwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota.+ Pakati pa mʼbadwo umenewu inu mukuwala ngati zounikira mʼdzikoli.+
15 Anthu akayatsa nyale saivindikira ndi dengu, koma amaiika pachoikapo nyale ndipo imaunikira onse mʼnyumbamo.+
21 Iye anawauzanso kuti: “Nyale saivindikira ndi dengu* kapena kuiika pansi pa bedi, amatero ngati? Koma amaiika pachoikapo nyale,+ si choncho kodi?
33 Munthu akayatsa nyale saiika pamalo obisika kapena kuivindikira ndi dengu,* koma amaiika pachoikapo nyale,+ kuti amene akulowa aone kuwala.
15 kuti mukhale opanda chifukwa chokunenezerani komanso osalakwa. Mukhale ana a Mulungu+ opanda chilema pakati pa mʼbadwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota.+ Pakati pa mʼbadwo umenewu inu mukuwala ngati zounikira mʼdzikoli.+