Mateyu 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atate wanga wapereka zinthu zonse kwa ine+ ndipo palibe amene akumudziwa bwino Mwana koma Atate okha.+ Komanso palibe amene akuwadziwa bwino Atate koma Mwana yekha ndi aliyense amene Mwanayo wafuna kumuululira za Atatewo.+ Yohane 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Palibe munthu amene anaonapo Mulungu ndi kale lonse,+ mulungu wobadwa yekha+ amene ali pambali pa Atate*+ ndi amene anafotokoza za Mulungu.+ Yohane 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ngati mmene zilili kuti Atate amandidziwa ndipo inenso ndimadziwa Atate.+ Choncho ndikupereka moyo wanga chifukwa cha nkhosazo.+
27 Atate wanga wapereka zinthu zonse kwa ine+ ndipo palibe amene akumudziwa bwino Mwana koma Atate okha.+ Komanso palibe amene akuwadziwa bwino Atate koma Mwana yekha ndi aliyense amene Mwanayo wafuna kumuululira za Atatewo.+
18 Palibe munthu amene anaonapo Mulungu ndi kale lonse,+ mulungu wobadwa yekha+ amene ali pambali pa Atate*+ ndi amene anafotokoza za Mulungu.+
15 ngati mmene zilili kuti Atate amandidziwa ndipo inenso ndimadziwa Atate.+ Choncho ndikupereka moyo wanga chifukwa cha nkhosazo.+