-
Luka 1:67Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
67 Ndiyeno Zekariya, bambo a mwanayo, anadzazidwa ndi mzimu woyera ndipo ananenera kuti:
-
-
Luka 3:3, 4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Choncho iye anapita mʼmidzi yonse yapafupi ndi Yorodano ndipo ankalalikira za ubatizo monga chizindikiro cha kulapa kuti machimo akhululukidwe.+ 4 Ankachita zimenezi mogwirizana ndi zimene zinalembedwa mʼbuku la mawu a Mneneri Yesaya kuti: “Winawake akufuula mʼchipululu kuti: ‘Konzani njira ya Yehova!* Muwongole misewu yake.+
-