-
2 Petulo 3:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Musatero ayi, koma muzichita zinthu zimene zingakuthandizeni kuti mupitirize kulandira kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye ndi Mpulumutsi wathu Yesu Khristu, ndiponso kuti mumudziwe bwino kwambiri. Kwa iye kukhale ulemerero, kuyambira panopa mpaka muyaya. Ame.
-