Salimo 118:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwala umene omanga nyumba anaukanaWakhala mwala wapakona* wofunika kwambiri.+ Yesaya 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndikuika mwala woyesedwa mu Ziyoni kuti ukhale maziko,+Umenewu ndi mwala wapakona wamtengo wapatali+ wa maziko olimba.+ Palibe munthu woukhulupirira amene adzade nkhawa.+ Mateyu 21:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “Paja Malemba amanena kuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.*+ Umenewu wachokera kwa Yehova* ndipo ndi wodabwitsa mʼmaso mwathu.+ Kodi simunawerenge zimeneziʼ? 1 Petulo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho iye ndi wamtengo wapatali kwa inu chifukwa mumamukhulupirira. Koma kwa amene samukhulupirira, “mwala umene omanga nyumba anaukana,+ wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.”+
16 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndikuika mwala woyesedwa mu Ziyoni kuti ukhale maziko,+Umenewu ndi mwala wapakona wamtengo wapatali+ wa maziko olimba.+ Palibe munthu woukhulupirira amene adzade nkhawa.+
42 Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “Paja Malemba amanena kuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.*+ Umenewu wachokera kwa Yehova* ndipo ndi wodabwitsa mʼmaso mwathu.+ Kodi simunawerenge zimeneziʼ?
7 Choncho iye ndi wamtengo wapatali kwa inu chifukwa mumamukhulupirira. Koma kwa amene samukhulupirira, “mwala umene omanga nyumba anaukana,+ wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.”+