-
Machitidwe 14:21, 22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Atalengeza uthenga wabwino mumzindawu nʼkuphunzitsa anthu ambiri ndithu kuti akhale ophunzira, anabwerera ku Lusitara, ku Ikoniyo ndi ku Antiokeya. 22 Mʼmalo onsewa ankalimbitsa ophunzira+ komanso kuwathandiza kuti apitirize kukhala ndi chikhulupiriro. Ankawauza kuti: “Tiyenera kukumana ndi mavuto ambiri kuti tikalowe mu Ufumu wa Mulungu.”+
-