-
Agalatiya 1:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Komabe, ngati ifeyo kapena mngelo wochokera kumwamba angalengeze nkhani ina kwa inu nʼkumanena kuti akulengeza uthenga wabwino, koma nkhaniyo nʼkukhala yosiyana ndi uthenga wabwino umene tinaulengeza kwa inu, ameneyo akhale wotembereredwa.
-