1 Akorinto 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma tsopano ndikukulemberani kuti musiye kugwirizana+ ndi aliyense wotchedwa mʼbale, amene ndi wachiwerewere* kapena wadyera,+ wopembedza mafano, wolalata, chidakwa+ kapenanso wolanda,+ ngakhale kudya naye munthu wotereyu ayi. Agalatiya 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano ntchito za thupi lochimwali zimaonekera mosavuta. Ntchito zimenezi ndi chiwerewere,*+ khalidwe limene limadetsa munthu, khalidwe lopanda manyazi,*+ Aefeso 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa mfundo iyi mukuidziwa ndipo mukuimvetsa bwino, kuti munthu wachiwerewere*+ kapena wodetsedwa kapena waumbombo,+ umene ndi kulambira mafano, sadzalowa mu Ufumu wa Khristu ndi wa Mulungu.+
11 Koma tsopano ndikukulemberani kuti musiye kugwirizana+ ndi aliyense wotchedwa mʼbale, amene ndi wachiwerewere* kapena wadyera,+ wopembedza mafano, wolalata, chidakwa+ kapenanso wolanda,+ ngakhale kudya naye munthu wotereyu ayi.
19 Tsopano ntchito za thupi lochimwali zimaonekera mosavuta. Ntchito zimenezi ndi chiwerewere,*+ khalidwe limene limadetsa munthu, khalidwe lopanda manyazi,*+
5 Chifukwa mfundo iyi mukuidziwa ndipo mukuimvetsa bwino, kuti munthu wachiwerewere*+ kapena wodetsedwa kapena waumbombo,+ umene ndi kulambira mafano, sadzalowa mu Ufumu wa Khristu ndi wa Mulungu.+