Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2007
Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo
BAIBULO
Baibulo Loyamba la Chipwitikizi, 7/1
Ernst Glück Anagwira Ntchito Yaikulu Zedi (kumasulira m’Chilativiya), 6/15
Inde, N’losavuta Kuwerenga, Koma Kodi N’lolondola? (Baibulo la Mphindi 100), 2/1
Kodi “Chipangano Chakale” Chinatha Ntchito? 9/1
Kodi Yesu Anali ndi Baibulo Lakelake, 12/1
Mabaibulo a Zinenero za mu Africa, 1/15
Malangizo Othandizadi, 4/1
Mapale Akale Amatsimikizira, 11/15
Mfundo Zazikulu za M’buku la Yesaya—Gawo 2, 1/15
Mfundo Zazikulu za M’buku la Yeremiya, 3/15
Mfundo Zazikulu za M’buku la Maliro, 6/1
Mfundo Zazikulu za M’buku la Ezekieli, 7/1, 8/1
Mfundo Zazikulu za M’buku la Danieli, 9/1
Mfundo Zazikulu za M’buku la Hoseya, 9/15
Mfundo Zazikulu za M’mabuku a Yoweli ndi Amosi, 10/1
Mfundo Zazikulu za M’mabuku a Obadiya, Yona, ndi Mika, 11/1
Mfundo Zazikulu za M’mabuku a Nahumu, Habakuku, ndi Zefaniya, 11/15
Mfundo Zazikulu za M’mabuku a Hagai ndi Zekariya, 12/1
Mfundo Zazikulu za m’Buku la Malaki, 12/15
Mmene Mipukutu Inafikira Pokhala Baibulo Lathunthu, 6/1
“Mphatso Yamtengo Wapatali” ya Anthu a ku Poland, 8/15
Ntchito ya Alembi Akale, 3/15
MAFUNSO OCHOKERA KWA OWERENGA
Ana achikhristu akaphunzitsidwa bwino, ndiye kuti basi sadzasiya njira ya Yehova? (Miy. 22:6), 6/1
Kapolo wokhulupirika ndi “wanzeru”? (Mt 24:45), 9/1
Kodi Akhristu ayenera kupewa mankhwala a caffeine? 4/15
Kodi kusankha Akhristu odzozedwa kunatha liti? 5/1
“Mwamuna mmodzi mwa chikwi”? (Mlal. 7:28), 1/15
Kodi ndani ankakolola barele woyamba kucha? 7/15
Kodi njoka inali ndi miyendo? (Ge 3:14), 6/15
Kodi “nkhondo ya Haramagedo n’chiyani, (Chiv. 16:14, 16), 2/1
Kodi Nowa analowetsa nyama zingati zodyedwa m’chingalawa? 3/15
Kodi Yakobo analakwa kunamizira kuti anali Esau? (Ge 27:18, 19), 10/1
Kumenyanitsa matambula, 2/15
Kusindikiza chisindikizo (Chiv. 7:3), 1/1
“Mkazi wa mwamuna mmodzi,” (1Ti 5:9), 4/1
Mkhristu wa Mboni za Yehova akakhale nawo pamwambo wa ukwati wa anthu omwe si Mboni? 11/15
N’chifukwa chiyani Sauli anafunsa funso limeneli? (1Sa 17:58), 8/1
N’chifukwa chiyani Yesu anagwiritsa ntchito vinyo? 9/15
Nkhani ya Kusaka Kapena Kusodza? 12/1
MBIRI YA MOYO WANGA
Anatipulumutsa ku Ulamuliro Wankhanza (H. Dornik), 9/1
Chifukwa Chimene Ndimasangalalira Kupanga Ophunzira (P. Moseley), 2/1
Kutumikira Yehova Ndi Mwayi Waukulu Koposa (Z. Stigers), 8/1
Kuyenda Molowera ku Dziko Latsopano (J. Pramberg), 12/1
Munthu Amene Ankakonda Moyo Ndiponso Anthu (D. Sydlik), 1/1
Ndadalitsidwa Moyo Wanga Wonse Chifukwa Chosankha Bwino Zochita (P. Kushnir), 1/1
Ndakhala Ndikudikirira Ufumu Womwe “Suli Mbali ya Dziko Lino” (N. Gutsulyak), 3/1
Ndinaphunzira Kukhulupirira Yehova ndi Mtima Wonse (A. Baxter), 11/1
Ntchito Yopanga Ophunzira Yakhudza Kwambiri Zochita Pamoyo Wanga (L. Peters), 4/1
Tikukondwera Chifukwa ‘Anapambana Limodzi ndi Mwanawankhosa’ (C. Barber), 10/15
Tinafunitsitsa Kukwaniritsa Utumiki (L. Davison), 6/1
Tinapeza Chuma Chimene Tinkafufuza (D. Smith ndi D. Ward), 5/1
MBONI ZA YEHOVA
Chikhulupiriro cha Mayi Wina Chinapambana, 8/1
Chitsanzo cha Kuona Mtima, 2/15
“Chonde Landirani Kamphatso Kangaka” (Russia), 11/15
Mavuto Popereka Uthenga Wabwino (Africa), 10/15
Mayi wa Zaka Zoposa 100 Ali ndi Cholinga Pamoyo, 1/15
Mipata Youza Ena Chikhulupiriro Chanu? (anzanu kusukulu), 11/1
Misonkhano Yachigawo ya Chipulumutso Chayandikira (2006), 7/1
Mlandu Unatikomera ku Khoti Lalikulu ku Ulaya (Russia), 5/15
“Mphatso Yabwino Kwambiri” (Belgium), 12/15
“Mwayera Kale Ndipo M’mofunika Kukolola,” (Guajira Peninsula) 4/15
“Ndinamusirira Chifukwa Sanasinthe Maganizo Ake” (Germany), 10/15
“Nyumba ya Miyala” (Zimbabwe), 2/15
Omaliza Maphunziro a Gileadi, 1/1, 7/1
“Siliva Ndi Wanga, Golidi Ndi Wanga” (zopereka), 11/1
“Tsatirani Khristu!” Msonkhano Wachigawo, 3/1
Wolemala Koma Wodzipereka, 4/15
Zimene Adryana Analakalaka, 4/15
“Zozizwitsa” Ziwiri pa Msonkhano Umodzi (Georgia), 8/1
MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU
Achinyamata Mumasangalatsa Mtima wa Makolo Anu, 5/1
“Anatiumiriza Kupita Basi!” 3/15
Kodi Mumangoganizira za Lero Zokha Basi? 10/15
Kodi Mumatsitsimula Ena? 11/15
Kodi Mungafutukule Chikondi Chanu? 1/1
Kodi Munthu Wauzimu Ndi Wotani? 8/1
Kodi Ndingatani Kuti Ndiphunzitse Bwino Ana Anga? 5/15
‘Kubala Zipatso Atakalamba,’ 9/15
Kukhulupirira Ulosi wa M’Baibulo, 4/1
Kunena Zoona? 2/1
Kupirira Zinthu Zopanda Chilungamo, 8/15
Kuwala N’kodabwitsa, 3/15
Lilime ndi Lamphamvu, 6/1
Londolani Kuwala, 10/15
Mdulidwe Umasonyeza Mwamuna Weniweni? 6/1
Mfundo Zodalirika Ndiponso Zosasinthasintha, 6/15
Moyo Wosangalala, 11/15
M’pofunika Kwambiri Kuyamikira Ena, 9/1
Mtima Wosamalira Ena, 6/15
Mungaphunzire Chiyani kwa Ana? 2/1
Musafooke Mwana Wanu Akapanduka, 1/15
Mwamuna ndi Mkazi Onse Ali ndi Udindo Wolemekezeka, 1/15
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kusonkhana? 5/15
‘Ndiyeseni, Yehova,’ 8/15
Nsembe Zokondweretsa Mulungu, 4/1
“Nzeru Itchinjiriza” (Miy. 16), 7/15
Osangalala Kudikira Yehova, 3/1
Phunzitsani Ana Anu Kukonda Mtendere, 12/1
Phunzitsani Ana Anu Kukonda Mulungu, 9/15
Sitiyenera Kuchita Zinthu Monyanyira? 2/15
Si Zimene Munali Kuyembekezera, 4/15
Sonyezani ‘Chifundo Chachikulu,’ 12/15
‘Valani Kudzichepetsa,’ 11/1
“Zolingalira Zako Zidzakhazikika” (Miy. 16), 5/15
Zosankha Zimene Zimabweretsa Chisangalalo, 10/1
NKHANI ZOPHUNZIRA
Achinyamata—Khalani ndi Zolinga Zolemekeza Mulungu, 5/1
Akazi, Muzilemekeza Kwambiri Amuna Anu, 2/15
Amuna, Muzitsanzira Umutu wa Khristu, 2/15
Ananu, Muzimvera Makolo Anu,” 2/15
‘Atate Wanu Ndi Wachifundo,’ 9/15
“Chenjerani ndi Kusirira kwa Nsanje kwa Mtundu Uliwonse,” 8/1
“Chirimikani, Ndipo Penyani Chipulumutso cha Yehova,” 12/15
“Iwe Uzikhala Wosangalala Basi” 1/1
Iwo Ndi Okalamba Koma Akubalabe Zipatso Zauzimu, 6/1
Khalani Okhulupirika kwa Khristu ndi kwa Kapolo Wake, 4/1
Kodi Inuyo Mumayembekezeradi Kuti Akufa Adzauka? 5/15
Kodi Muli ku Mbali ya Ulamuliro wa Yehova? 12/1
Kodi ‘Mupitiriza Kuyenda mwa Mzimu’? 7/15
Kodi Mwachimwira Mzimu Woyera? 7/15
Kodi Mwakonzekera Tsiku la Yehova? 12/15
Kodi Ndinu “Wolemera kwa Mulungu”? 8/1
Kodi Tingasonyeze Bwanji Chifundo? 9/15
Kodi Ziwanda Tingalimbane Nazo Bwanji? 3/15
Kuchita Chifuniro cha Mulungu Masiku Ano, 10/1
Kufufuza “Zinthu Zozama za Mulungu,” 11/1
Kufunafuna Cholinga Chabwino Pamoyo, 10/1
Kupirira Mavuto Kuli Ndi Ubwino Wake, 8/15
Kupulumutsidwa ku Misampha ya Wosaka Mbalame, 10/1
“Kuuka Koyamba” Kuli M’kati Panopa! 1/1
Lolani Mawu a Mulungu Kutsogolera Mapazi Anu, 5/1
Makhalidwe Okuthandizani Kupanga Ophunzira, 11/15
Makolo Phunzitsani Ana Anu Mwachikondi, 9/1
Mavuto Onse Adzatha Posachedwapa, 5/15
Mawu A Yehova Amakwaniritsidwa Nthawi Zonse, 11/1
Mpingo Uyenera Kulimbikitsidwa, 4/15
Mpingo Uyenera Kutamanda Yehova, 4/15
“Musabwezere Choipa pa Choipa,” 7/1
Musalekanitse Chimene Mulungu Anachimanga Pamodzi, 5/1
Musasiye Kukhala Oyamikira, 2/1
Mverani Chikumbumtima Chanu, 10/15
Okalamba Ndi Dalitso kwa Anthu Ocheperapo Msinkhu, 6/1
Opani Yehova Kuti Mukhale ndi Moyo Wosangalala, 3/1
Palibe Chida Chosulidwira Inu Chimene Chidzapambane, 12/15
Phunzitsani Ana Anu Kukonda Yehova, 9/1
Phunzitsani Zimene Baibulo Limaphunzitsa Kwenikweni, 1/15
Pirirani Poyembekezera Tsiku la Yehova, 7/15
“Pitirizani Kugonjetsa Choipa mwa Kuchita Chabwino,” 7/1
Thandizani Anthu Kumvera Zimene Baibulo Limaphunzitsa, 1/15
Tikweze Dzina la Yehova Pamodzi, 3/1
‘Tinapangidwa Modabwitsa,’ 6/15
Tizigonjera Abusa Achikondi Modzichepetsa, 4/1
Tsanzirani Wopanga Ophunzira Waluso, 11/15
Tsatirani Chikumbumtima Chanu, 10/15
Ulamuliro wa Yehova ndi Ufumu wa Mulungu, 12/1
Yehova Amakonda Chilungamo, 8/15
Yehova Amakondwera Mukamamumvera, 6/15
Yehova Ndi Mulungu Woyamikira, 2/1
NKHANI ZOSIYANASIYANA
“Anamanga Nyumba ya Isiraeli (Leya, Rakele), 10/1
Barizilai, 7/15
Bereya, 4/15
Buku la John Milton, 9/15
Chikhristu Chifalikira ku Asia Minor, 8/15
Chikondwerero cha Chikunja Chingakhale cha Chikhristu? 12/15
“Choonadi N’chiyani?” 10/1
Hana, 3/15
Jonatani Anachita Zinthu Mothandizidwa ndi Mulungu, 9/15
Kalendala Zaulimi ya mu “Dziko Lokoma,” 6/15
Kodi Muli ndi Mlangizi pa Zauzimu? 12/15
Kodi Mumaopa Zam’tsogolo? 5/15
Kodi Mzimu wa Munthu Sufa? 7/15
Kodi Nkhanza Zidzathadi? 4/15
Kodi N’zotheka Anthu Padziko Lonse Kugwirizana? 12/1
Kodi Tsankho Lingathe Bwanji? 7/1
Kodi Zoipa Zingathetsedwe? 6/1
Kulemba Kunali Kofunika Kwambiri ku Isiraeli, 8/15
Kulimbikitsa Makolo Oferedwa, 5/1
Luka Wantchito Mnzake Wokondedwa wa Paulo, 11/15
“Mboni Yokhulupirika Kuthambo,” 7/15
M’dziwe la Siloamu,” 7/15
Mungadziwe Kupembedza Koona? 3/1
Munthu Zikumuyendera Bwino? 1/1
Muyenera Kusamala Posankha Chipembedzo? 3/1
Samueli Analimbikitsa Kulambira Koona, 1/15
Sangalalani ndi Dziko Lapansi Lokongolali, 2/15
Saulo ndi Anzake Ndiponso Adani Ake, 6/15
Surakusa Mzinda Womwe Paulo Anaima Paulendo Wake, 10/15
Wessel Gansfort “Anali ndi Mfundo Zosintha Zinthu,” 3/1
“Ambuye, N’chifukwa Chiyani Simunachitepo Kanthu?” (Papa ku Auschwitz), 5/15
Amosi—Wotchera Nkhuyu Kapena Wobaya Nkhuyu? 2/1
Yefita Anasunga Chowinda Chake kwa Yehova, 5/15
“Zombo za ku Kitimu” Panyanja, 10/15
YEHOVA
Dzina la Mulungu mu Nyimbo za ku Russia, 9/1
Kodi Chilengedwe N’chopandadi Mlengi? 8/15
Kodi Mulungu Amakuonani? 8/1
N’chifukwa Chiyani Mulungu Walola Kuti Zoipa Zizichitika? 9/15
YESU KRHISTU
Zinthu Zimene Khristu Adzachita Akabwera, 3/15