Mateyu 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Atafika kutsidya linalo, mʼdera la Agadara, anakumana ndi amuna awiri ogwidwa ndi ziwanda akuchokera mʼmanda.*+ Amunawa anali ochititsa mantha kwambiri moti panalibe aliyense amene ankalimba mtima kudutsa msewu umenewo. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:28 Yesu—Ndi Njira, tsa. 114 Nsanja ya Olonda,12/1/1997, tsa. 57/15/1992, tsa. 65/15/1987, tsa. 26
28 Atafika kutsidya linalo, mʼdera la Agadara, anakumana ndi amuna awiri ogwidwa ndi ziwanda akuchokera mʼmanda.*+ Amunawa anali ochititsa mantha kwambiri moti panalibe aliyense amene ankalimba mtima kudutsa msewu umenewo.