Maliko 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Komanso pa nthawiyo, munthu akadzakuuzani kuti, ‘Onani! Khristu uja ali kuno,’ kapena, ‘Onani! Ali uko,’ musadzakhulupirire zimenezo.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:21 Nsanja ya Olonda,2/15/1994, ptsa. 11-12
21 Komanso pa nthawiyo, munthu akadzakuuzani kuti, ‘Onani! Khristu uja ali kuno,’ kapena, ‘Onani! Ali uko,’ musadzakhulupirire zimenezo.+