Levitiko 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Choncho Aroni azipereka ng’ombe yamphongo ya nsembe yake yamachimo, kuti aphimbe machimo ake ndi a nyumba yake. Akatero azipha ng’ombe ya nsembe yake yamachimoyo.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:11 Nsanja ya Olonda,2/15/1998, ptsa. 12, 17
11 “Choncho Aroni azipereka ng’ombe yamphongo ya nsembe yake yamachimo, kuti aphimbe machimo ake ndi a nyumba yake. Akatero azipha ng’ombe ya nsembe yake yamachimoyo.+