36 Kutinso azibweretsa ana aamuna oyamba kubadwa+ mwa ana athu ndi ziweto+ zathu malinga ndi zolembedwa m’chilamulo.+ Komanso kuti azibweretsa ana oyamba kubadwa a ng’ombe ndi nkhosa+ zathu kunyumba ya Mulungu wathu, kwa ansembe amene anali kutumikira m’nyumba ya Mulungu wathu.+