Salimo 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amadikirira anthu pamalo obisika ngati mkango pamalo ake obisalapo.+Amawadikirira+ kuti atenge mokakamiza munthu wosautsika.Amakulunga wosautsika mu ukonde wake ndi kumutenga mokakamiza.+
9 Amadikirira anthu pamalo obisika ngati mkango pamalo ake obisalapo.+Amawadikirira+ kuti atenge mokakamiza munthu wosautsika.Amakulunga wosautsika mu ukonde wake ndi kumutenga mokakamiza.+