Yesaya 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Uwu ndi uthenga wokhudza Mowabu:+ Chifukwa chakuti wasakazidwa usiku, Ari+ wa ku Mowabu wakhala chete. Chifukwa chakuti wasakazidwa usiku, Kiri+ wa ku Mowabu wakhala chete. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:1 Yesaya 1, tsa. 193
15 Uwu ndi uthenga wokhudza Mowabu:+ Chifukwa chakuti wasakazidwa usiku, Ari+ wa ku Mowabu wakhala chete. Chifukwa chakuti wasakazidwa usiku, Kiri+ wa ku Mowabu wakhala chete.