Zekariya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndakwiyira kwambiri anthu a mitundu ina amene akukhala mwabata.+ Ndawakwiyira chifukwa chakuti ine ndinangokwiyira anthu anga pang’ono pokha,+ koma anthu amenewa anakulitsa tsoka la anthu angawo.”’+
15 Ndakwiyira kwambiri anthu a mitundu ina amene akukhala mwabata.+ Ndawakwiyira chifukwa chakuti ine ndinangokwiyira anthu anga pang’ono pokha,+ koma anthu amenewa anakulitsa tsoka la anthu angawo.”’+