Mateyu 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Fosholo yake youluzira mankhusu* ili m’manja mwake, ndipo malo ake opunthirapo mbewu adzawayeretseratu kuti mbee! Tirigu adzamututira m’nkhokwe,+ koma mankhusu adzawatentha+ ndi moto umene sungazimitsidwe.” Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:12 Nsanja ya Olonda,5/1/2012, tsa. 306/15/1987, ptsa. 16, 19-20
12 Fosholo yake youluzira mankhusu* ili m’manja mwake, ndipo malo ake opunthirapo mbewu adzawayeretseratu kuti mbee! Tirigu adzamututira m’nkhokwe,+ koma mankhusu adzawatentha+ ndi moto umene sungazimitsidwe.”