14 Kanotu ndi kachitatu+ kukhala wokonzeka kubwera kwa inu, koma sindidzakhala katundu wolemetsa. Pakuti sindikufuna zinthu zanu,+ koma inuyo. Paja ana+ sayenera kusunga chuma kuti chidzathandize makolo awo m’tsogolo, koma makolo ndi amene ayenera kusungira ana awo.+