1 Petulo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 monga mmene Sara analili womvera kwa Abulahamu, ndipo anali kumutcha kuti “mbuyanga.”+ Tsopano inuyo mwakhala ana ake, ndipo mukhalabe ana ake mukapitiriza kuchita zabwino ndi kusaopa chochititsa mantha chilichonse.+ 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:6 Nsanja ya Olonda,3/1/2005, ptsa. 19-205/15/2004, tsa. 26
6 monga mmene Sara analili womvera kwa Abulahamu, ndipo anali kumutcha kuti “mbuyanga.”+ Tsopano inuyo mwakhala ana ake, ndipo mukhalabe ana ake mukapitiriza kuchita zabwino ndi kusaopa chochititsa mantha chilichonse.+