2 Samueli 22:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Yehova ndi wamoyo.+ Lidalitsike Thanthwe langa.+Mulungu wanga, thanthwe limene limandipulumutsa likhale lokwezeka.+ Salimo 99:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kwezani Yehova Mulungu wathu+ ndipo muweramireni pachopondapo mapazi ake.+Iye ndi woyera.+ Yesaya 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Inu Yehova, ndinu Mulungu wanga.+ Ndikukukwezani+ ndi kutamanda dzina lanu+ chifukwa mwachita zinthu zabwino kwambiri.+ Mwakwaniritsa zolinga zanu+ zakalekale ndipo mwachita zinthu mokhulupirika+ ndi modalirika.+
47 Yehova ndi wamoyo.+ Lidalitsike Thanthwe langa.+Mulungu wanga, thanthwe limene limandipulumutsa likhale lokwezeka.+
25 Inu Yehova, ndinu Mulungu wanga.+ Ndikukukwezani+ ndi kutamanda dzina lanu+ chifukwa mwachita zinthu zabwino kwambiri.+ Mwakwaniritsa zolinga zanu+ zakalekale ndipo mwachita zinthu mokhulupirika+ ndi modalirika.+