Oweruza 6:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Choncho Yowasi anatcha Gidiyoni dzina lakuti Yerubaala*+ pa tsiku limenelo, ndipo anati: “Baala adziweruzire yekha mlandu, chifukwa winawake wagwetsa guwa lake lansembe.”+ Oweruza 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako amuna a Isiraeli anauza Gidiyoni kuti: “Ukhale wotilamulira wathu,+ iweyo, mwana wako ndi mdzukulu wako, chifukwa watipulumutsa m’manja mwa Amidiyani.”+ 1 Samueli 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Yehova anatumiza Yerubaala,+ Bedani, Yefita+ ndi Samueli+ ndipo anakulanditsani m’manja mwa adani anu onse okuzungulirani, kuti mukhale popanda chokuopsani.+ Aheberi 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Nanga ndinenenso chiyani pamenepa? Nthawi indichepera kuti ndipitirize kufotokoza za Gidiyoni,+ Baraki,+ Samisoni,+ Yefita,+ Davide,+ komanso Samueli+ ndi aneneri enanso.+
32 Choncho Yowasi anatcha Gidiyoni dzina lakuti Yerubaala*+ pa tsiku limenelo, ndipo anati: “Baala adziweruzire yekha mlandu, chifukwa winawake wagwetsa guwa lake lansembe.”+
22 Kenako amuna a Isiraeli anauza Gidiyoni kuti: “Ukhale wotilamulira wathu,+ iweyo, mwana wako ndi mdzukulu wako, chifukwa watipulumutsa m’manja mwa Amidiyani.”+
11 Pamenepo Yehova anatumiza Yerubaala,+ Bedani, Yefita+ ndi Samueli+ ndipo anakulanditsani m’manja mwa adani anu onse okuzungulirani, kuti mukhale popanda chokuopsani.+
32 Nanga ndinenenso chiyani pamenepa? Nthawi indichepera kuti ndipitirize kufotokoza za Gidiyoni,+ Baraki,+ Samisoni,+ Yefita,+ Davide,+ komanso Samueli+ ndi aneneri enanso.+