1 Samueli 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano pita ukaphe Aamaleki+ ndi kuwawononga+ pamodzi ndi zonse zimene ali nazo. Usakawamvere chisoni, ukawaphe ndithu. Ukaphe+ mwamuna ndi mkazi, mwana wamng’ono ndi mwana woyamwa,+ ng’ombe ndi nkhosa, ngamila ndi bulu.’”+ Yobu 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi si paja wochita zoipa amakumana ndi zosautsa,+Ndipo ochitira anzawo zopweteka tsoka limawagwera? Miyambo 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Njira ya Yehova ndiyo malo achitetezo kwa munthu wopanda cholakwa,+ koma anthu ochita zopweteka ena adzawonongedwa.+ Miyambo 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsoka limatsatira ochimwa,+ koma olungama ndi amene amalandira mphoto zabwino.+
3 Tsopano pita ukaphe Aamaleki+ ndi kuwawononga+ pamodzi ndi zonse zimene ali nazo. Usakawamvere chisoni, ukawaphe ndithu. Ukaphe+ mwamuna ndi mkazi, mwana wamng’ono ndi mwana woyamwa,+ ng’ombe ndi nkhosa, ngamila ndi bulu.’”+
3 Kodi si paja wochita zoipa amakumana ndi zosautsa,+Ndipo ochitira anzawo zopweteka tsoka limawagwera?
29 Njira ya Yehova ndiyo malo achitetezo kwa munthu wopanda cholakwa,+ koma anthu ochita zopweteka ena adzawonongedwa.+